Yeremiya 33:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzautengera moyo ndi kuuciritsa, ndi kuwaciritsa; ndipo ndidzawaululira iwo kucuruka kwa mtendere ndi zoona.

Yeremiya 33

Yeremiya 33:5-16