Yeremiya 33:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adza kumenyana ndi Akasidi, koma adzangozidzaza ndi mitembo ya anthu, amene ndawapha m'mkwiyo wanga ndi mu ukali wanga, amene ndabisira mudzi uno nkhope yanga cifukwa ca zoipa zao zonse.

Yeremiya 33

Yeremiya 33:1-7