Yeremiya 33:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo pangano langa lidzasweka ndi Davide mtumiki wanga, kuti asakhale ndi mwana wamwamuna wakulamulira pa mpando wa ufumu wace; ndiponso ndi Alevi ansembe, atumiki anga.

Yeremiya 33

Yeremiya 33:14-26