Yeremiya 31:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Ngati ukhoza kuyesa thambo la kumwamba, ndi kusanthula pansi maziko a dziko, pamenepo ndidzacotsa mbeu zonse za Israyeli cifukwa ca zonse anazicita, ati Yehova.

Yeremiya 31

Yeremiya 31:29-38