Yeremiya 31:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati malembawa acoka pamaso panga, ati Yehova, pamenepo mbeunso ya Israyeli idzaleka kukhala mtundu pamaso panga ku nthawi zonse.

Yeremiya 31

Yeremiya 31:27-40