Yeremiya 30:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkwiyo waukali wa Yehova sudzabwerera, mpaka wacita, mpaka watha zomwe afuna kucita m'mtima mwace: masiku akumariza mudzacizindikira.

Yeremiya 30

Yeremiya 30:19-24