Yeremiya 30:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, cimphepo ca Yehova, kupsya mtima kwace, caturuka, cimphepo cakukokolola: cidzagwa pamtu pa oipa.

Yeremiya 30

Yeremiya 30:13-24