Yeremiya 30:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mabwenzi ako onse anakuiwala iwe; salikukufuna iwe; pakuti ndakulasa ndi bala la mdani, ndi kulanga kwa wankhanza; cifukwa ca mphulupulu yako yaikuru, cifukwa zocimwa zako zinacuruka.

Yeremiya 30

Yeremiya 30:11-19