Yeremiya 23:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akadaima m'upo wanga, akadamvetsa anthu anga mau anga, akadatembenuza iwo ku njira yao yoipa, ndi ku coipa ca nchito zao.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:16-25