Yeremiya 23:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sindinatuma aneneri awa, koma anathamanga; sindinanena ndi iwo, koma ananenera.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:18-28