Yeremiya 22:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi udzakhala mfumu, cifukwa iwe uyesa kuposa ena ndi mikungudza? Kodi atate wako sanadya ndi kumwa, ndi kuweruza molungama? kumeneko kunamkomera.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:5-24