Yeremiya 22:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene ati, Ndidzadzimangira ndekha nyumba yotakata ndi zipinda zapamwamba zazikuru, nadziboolera mazenera; nabvundima chindwi lam'kati ndi mikungudza, naipaka ndi utoto wofiira.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:9-17