Yeremiya 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cimo la Yuda lalembedwa ndi peni lacitsulo, ndi nsonga ya diamondi; lalembedwa pa colembapo ca m'mtima mwao, ndi pa nyanga za maguwa a nsembe anu.

Yeremiya 17

Yeremiya 17:1-3