Yeremiya 16:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, taonani, ndidzadziwitsa iwo kamodzi aka, ndidzawadziwitsa dzanja langa ndi mphamvu yanga; ndipo adzadziwa kuti dzina langa ndine Yehova.

Yeremiya 16

Yeremiya 16:20-21