Yeremiya 16:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akuru ndi ang'onong'ono adzafa m'dziko muno; sadzaikidwa, anthu sadzacita maliro ao, sadzadziceka, sadzadziyeseza adazi, cifukwa ca iwo;

Yeremiya 16

Yeremiya 16:1-15