Yeremiya 14:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musatinyoze ife, cifukwa ca dzina lanu; musanyazitse mpando wacifumu wa ulemerero wanu; mukumbukire musasiye pangano lanu lopangana ndi ife.

Yeremiya 14

Yeremiya 14:17-22