Yeremiya 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikaturukira kumunda, taonani ophedwa ndi lupanga! ndikalowa m'mudzi, taonani odwala ndi njala pakuti mneneri ndi wansembe ayendayenda m'dziko osadziwa kanthu.

Yeremiya 14

Yeremiya 14:10-21