Yeremiya 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova wa makamu, amene anakuoka iwe, wakunenera iwe coipa, cifukwa ca zoipa za nyumba ya Israyeli ndi nyumba ya Yuda, zimene anadzicitira okha pakuutsa mkwiyo wanga m'mene anafukizira Baala.

Yeremiya 11

Yeremiya 11:7-20