Yeremiya 10:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsanulirani ukali wanu pa amitundu osakudziwani Inu, ndi pa mabanja osaitana dzina lanu; pakuti anadya Yakobo, inde, anamudya namutha, napasula mokhalamo mwace.

Yeremiya 10

Yeremiya 10:18-25