Yakobo 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Khalani osautsidwa, lirani, lirani misozi; kuseka kwanu kusanduke kulira, ndi cimwemwe canu cisanduke cisoni.

Yakobo 4

Yakobo 4:4-17