Yakobo 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yandikirani kwa Mulungu, ndipo adzayandikira kwa inu, Sambani m'manja, ocimwa inu; yeretsani mitima, a mitima iwiri inu.

Yakobo 4

Yakobo 4:1-10