Oweruza 9:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Gaala anapenya anthuwo anati kwa Zebuli, Taona, alikutsika anthu kucokera pamwamba pa mapiri, Koma Zebuli ananena naye, Uona mthunzi wa mapiri ndi kuyesa anthu.

Oweruza 9

Oweruza 9:29-39