Oweruza 9:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Gaala mwana wa Ebedi anaturuka, naima polowera pa cipata ca mudzi; nauka Abimeleki ndi anthu anali naye m'molalira.

Oweruza 9

Oweruza 9:32-42