Oweruza 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, ngati mwacita moona ndi mwangwiro pakulonga Abimeleki ufumu, ngatinso mwamcitira cokoma Yerubaala ndi nyumba yace, ndi kumcitira monga anayenera manja ace;

Oweruza 9

Oweruza 9:9-19