Oweruza 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nkandankhuku unati kwa mitengo, Mukandidzoza mfumu yanu moonadi, tiyeni, thawirani ku mthunzi wanga; mukapanda kutero uturuke mota m'nkandankhuku ndi kunyeketsa mikungudza ya Lebano.

Oweruza 9

Oweruza 9:14-21