Oweruza 7:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagwira akalonga awiri a Midyani, Orebi ndi Zeebi; namupha Orebi ku thanthwe la Orebi; ndi Zeebi anamupha ku coponderamo mphesa ca Zeebi, nalondola Amidyani; ndipo anadza nayo mitu ya Orebi ndi Zeebi kwa Gideoni tsidya lija la Yordano.

Oweruza 7

Oweruza 7:17-25