Oweruza 7:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Gideoni ndi amuna zana anali naye anafikira ku cilekezero ca misasa poyambira ulonda wa pakati, atasintha alonda tsopano apa; ndipo anaomba malipenga, naphwanya mbiya zokhala m'manja mwao.

Oweruza 7

Oweruza 7:14-25