Oweruza 7:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakumva Gideoni kufotokozera kwa lotolo ndi tanthauzo lace, anadziwerama; nabwera ku misasa ya Israyeli nati, Taukani, pakuti Yehova wapereka a m'misasa a Midyani m'dzanja lanu.

Oweruza 7

Oweruza 7:14-20