Oweruza 6:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuuka mamawa amuna a ku mudziwo, taonani, guwa la nsembe la Baala litagamuka, ndi cifanizo cinali pomwepo citalikhidwa ndi ng'ombe yaciwiri yoperekedwa pa guwa la nsembe adalimanga.

Oweruza 6

Oweruza 6:24-29