Oweruza 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anawagulitsa m'dzanja la Yabini mfumu ya Kanani, wocita ufumu ku Hazori; kazembe wace wa nkhondo ndiye Sisera, wokhala ku Haroseti wa amitundu.

Oweruza 4

Oweruza 4:1-9