Oweruza 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali m'mawa mwace, anthu analawirira mamawa namangako guwa la nsembe, napereka nsembe zopsereza ndi nsembe zoyamika.

Oweruza 21

Oweruza 21:1-14