Oweruza 20:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amuna a Israyeli anabwereranso kwa ana a Benjamini, nawakantha ndi lupanga lakuthwa a m'mudzi wonse, ndi zoweta, ndi zonse adazipeza; anatenthanso midzi yonse anaipeza.

Oweruza 20

Oweruza 20:40-48