Oweruza 20:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mlevi, mwamuna wa mkazi anaphedwayo, anayankha nati, Ndinadza ine ku Gibeya wa Benjamini, ine ndi mkazi wanga wamng'ono, kugonako.

Oweruza 20

Oweruza 20:1-12