Oweruza 20:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Benjamini anamva kuti ana a Israyeli adakwera kumka ku Mizipa, Nati ana a Israyeli, Nenani, coipa ici cinacitika bwanji?

Oweruza 20

Oweruza 20:1-11