Oweruza 19:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nakhala pansi nadya namwa onse awiri pamodzi; nati kwa munthuyo atate wa mkaziyo, Ubvomere, ugone kuno usiku, nusekerere mtima wako.

Oweruza 19

Oweruza 19:1-11