Oweruza 19:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, tsiku lacinai, analawirira mamawa, nanyamuka iye kucoka; koma atate wa mkaziyo anati kwa mkamwini wace, Limbitsa mtima wako ndi mkate pang'ono, ndipo utatero upite.

Oweruza 19

Oweruza 19:1-7