Oweruza 19:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pofika iwo pa Yebusi linalimkulowa dzuwa, ndi mnyamata anati kwa mbuye wace, Tiyeni, tipambukire mudzi uwu wa Ayebusi ndi kugona pomwepa.

Oweruza 19

Oweruza 19:4-15