Oweruza 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma munthuyo anakana kugonako usiku, nanyamuka, nacoka, nadza pandunji pa Yebusi (ndiwo Yerusalemu); ndi pamodzi naye panali aburu awiri omangirira mbereko; anali nayenso mkazi wace wamng'ono.

Oweruza 19

Oweruza 19:1-12