Oweruza 17:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Ndipo Mika anamninkha zansembe Mleviyo, ndi mnyamatayo anakhala wansembe wace, nakhala m'nyumba ya Mika.

13. Nati Mika, Tsopano ndidziwa kuti Yehova adzandicitira cokoma, popeza ndiri naye Mlevi akhale wansembe wanga.

Oweruza 17