Ndipo Mika anamninkha zansembe Mleviyo, ndi mnyamatayo anakhala wansembe wace, nakhala m'nyumba ya Mika.