Oweruza 16:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakukondwera mitima yao, anati, Kaitaneni Samsoni, atisewerere. Naitana Samsoni m'kaidi; nasewera iye pamaso pao; ndipo anamuika iye pakati pa mizati.

Oweruza 16

Oweruza 16:22-30