Oweruza 16:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakumuona anthu analemekeza mulungu wao, pakuti anati, Mulungu wathu wapereka m'dzanja lathu mdani wathu, ndiye wakupasula dziko lathu, amene anatiphera ambiri.

Oweruza 16

Oweruza 16:23-30