Oweruza 16:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Delila anati kwa Samsoni, Mpaka tsopano wandipusitsa, ndi kundiuza mabodza; undiuze cimene angakumange naco. Nanena naye, Ukaomba njombi zisanu ndi ziwiri za pamutu panga mwa thonje loyala ndiko.

Oweruza 16

Oweruza 16:8-20