Oweruza 16:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Delila anatenga nsinga zatsopano, nammanga nazo, nanena naye, Atilisti akugwera, Samsoni. Ndi omlalira analikulinda m'cipinda ca m'kati. Koma anazidula pa manja ace ngati thonje.

Oweruza 16

Oweruza 16:10-22