Oweruza 15:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Iai, koma kumanga tidzakumanga, ndi kukupereka m'dzanja lao; koma kupha sitikupha iwe. Nammanga iye ndi zingwe ziwiri zatsopano, nakwera naye kucokera kuthanthwe.

Oweruza 15

Oweruza 15:9-20