Oweruza 14:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anatsikira Samsoni, ndi atate wace ndi mai wace ku Timna, nadza ku minda yamphesa ya Timna; ndipo taona, mwana wa mkango wakomana naye namdzumira.

Oweruza 14

Oweruza 14:1-13