Oweruza 14:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma atate wace ndi amai wace sanadziwa kuti cidacokera kwa Yehova ici; popeza analikufuna kutola cifukwa ndi Afilisti. Ndipo nthawi ija Afilisti analamulira Israyeli.

Oweruza 14

Oweruza 14:2-6