Oweruza 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wa Yehova sanaonekeranso kwa Manowa kapena kwa mkazi wace. Pamenepo anadziwa Manowa kuti ndiye mthenga wa Yehova.

Oweruza 13

Oweruza 13:16-25