Oweruza 13:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanyamuka Manowa natsata mkazi wace, namdzera mwamuna uja, nanena naye, Kodi ndinu mwamuna ujamunalankhulandimkaziyu? Ndipo anati, Ndine amene.

Oweruza 13

Oweruza 13:8-13