Oweruza 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo anafulumira nathamanga, nauza mwamuna wace, nanena naye, Taona, wandionekera munthu anandidzerayo tsiku lija.

Oweruza 13

Oweruza 13:9-20